Sangala-Diva-Gently-Chisomo-Sangala

 

LILONGWE-(MaraviPost)-Diva wina yemwe amaziwika ndi dzina loti Chisomo Sangala ali mmanja mwa apolisi aku Area 18 mumzinda mwa Lilongwe pomuganizira kuti analuma mnzake diso.

Mnzake wolumidwayu ndi Mercy Maulana yemwe anavulazidwa mwakuti nkhope yake silibwino konse.

Malinga ndi apolice, chipongwechi chinachitika kucha kwa lachinayi mamawa sabata latha.

Mercy-Maulana-alumidwa-nkhope-ndi-Diva-Chisomo-Sangala

 

Ndipo Diva Chisomo Gently analima Mercy Maulana mwakuti padakali pano nsikana olumidwayo sakuona ndipo pali chiwopsezo choti kudzakhala kovuta kuwonanso.

Padakali pano amangidwa Ali muchitokosi Ku area 18 police kudikila siku lomwe mulandu uzalowe mu Court.

: