Site icon The Maravi Post

“Mtengo wotsika wa feteleza ndilengeza mawa madzulo”-Chakwera

BLANTYRE-(MaraviPost)-Mtsogoleri wadziko lino Komanso wa chipani cha Malawi Congress (MCP) Lazarus Chakwera wati alengeza mtengo otsika wafeteleza mawa madzulo.

Chakwera wayankhula izi pa Mjamba mu mzinda wa Blantyre komwe chipanichi chikuchititsa msokhano okopa anthu kuti azachivotele pa chisankho chapa 16 September.

Mtsogoleriyu wati dziko la Malawi alinawo malingaliro oposela anayi kuphatikizapo kulimbikitsa ulimi wathilira akapambana pa 16 September.

aChakwera anauza anthu kuti alindikuthekera kokonzanso chuma chadziko lino kudzera ku ulimi.

Exit mobile version